Luka 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anapita ku Nazareti+ kumene anakulira. Mogwirizana ndi chizolowezi chake pa tsiku la Sabata, analowa mʼsunagoge+ nʼkuimirira kuti awerenge Malemba.
16 Kenako anapita ku Nazareti+ kumene anakulira. Mogwirizana ndi chizolowezi chake pa tsiku la Sabata, analowa mʼsunagoge+ nʼkuimirira kuti awerenge Malemba.