Yohane 6:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iwo anayamba kunena kuti: “Kodi uyu si Yesu mwana wa Yosefe, amene bambo ake ndi mayi ake tikuwadziwa?+ Nanga bwanji pano akunena kuti, ‘Ndinachokera kumwambaʼ?” Yohane 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ayudawo anadabwa nʼkufunsa kuti: “Kodi munthu ameneyu Malemba+ amenewa anawadziwa* bwanji, popeza sanapite kusukulu?”*+
42 Iwo anayamba kunena kuti: “Kodi uyu si Yesu mwana wa Yosefe, amene bambo ake ndi mayi ake tikuwadziwa?+ Nanga bwanji pano akunena kuti, ‘Ndinachokera kumwambaʼ?”
15 Ayudawo anadabwa nʼkufunsa kuti: “Kodi munthu ameneyu Malemba+ amenewa anawadziwa* bwanji, popeza sanapite kusukulu?”*+