Mateyu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukalowa mumzinda kapena mʼmudzi uliwonse, muzifufuza yemwe ali woyenerera kumuuza uthenga wanu, ndipo muzikhala mʼnyumba yake mpaka nthawi yochoka.+
11 Mukalowa mumzinda kapena mʼmudzi uliwonse, muzifufuza yemwe ali woyenerera kumuuza uthenga wanu, ndipo muzikhala mʼnyumba yake mpaka nthawi yochoka.+