Yakobo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umakhulupirira kuti kuli Mulungu mmodzi, si choncho? Ukuchita bwino. Komatu ziwanda nazonso zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera.+
19 Umakhulupirira kuti kuli Mulungu mmodzi, si choncho? Ukuchita bwino. Komatu ziwanda nazonso zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera.+