Deuteronomo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Ngati mwamuna wakwatira mkazi koma mkaziyo sakumusangalatsa chifukwa wamupeza ndi vuto linalake, azimulembera kalata yothetsera ukwati+ nʼkumupatsa, ndipo azimuchotsa panyumba pake.+ Mateyu 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pajanso anati: ‘Aliyense amene akuthetsa ukwati ndi mkazi wake, azipatsa mkaziyo kalata yothetsera ukwati.’+ Mateyu 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anamufunsa kuti: “Nanga nʼchifukwa chiyani Mose analamula kuti mwamuna azipereka kalata yothetsera ukwati kwa mkazi nʼkumusiya?”+
24 “Ngati mwamuna wakwatira mkazi koma mkaziyo sakumusangalatsa chifukwa wamupeza ndi vuto linalake, azimulembera kalata yothetsera ukwati+ nʼkumupatsa, ndipo azimuchotsa panyumba pake.+
31 Pajanso anati: ‘Aliyense amene akuthetsa ukwati ndi mkazi wake, azipatsa mkaziyo kalata yothetsera ukwati.’+
7 Iwo anamufunsa kuti: “Nanga nʼchifukwa chiyani Mose analamula kuti mwamuna azipereka kalata yothetsera ukwati kwa mkazi nʼkumusiya?”+