Aroma 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati mkaziyo angakwatiwe ndi mwamuna wina mwamuna wake ali moyo, ndiye kuti wachita chigololo.+ Koma ngati mwamuna wake wamwalira, mkaziyo wamasuka ku lamulo lokhudza mwamuna wake, choncho sanachite chigololo ngati atakwatiwa ndi mwamuna wina.+
3 Ngati mkaziyo angakwatiwe ndi mwamuna wina mwamuna wake ali moyo, ndiye kuti wachita chigololo.+ Koma ngati mwamuna wake wamwalira, mkaziyo wamasuka ku lamulo lokhudza mwamuna wake, choncho sanachite chigololo ngati atakwatiwa ndi mwamuna wina.+