Mateyu 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, mukapanda kutembenuka*+ nʼkukhala ngati ana aangʼono, simudzalowa mu Ufumu wakumwamba.+ Luka 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndithu ndikukuuzani, aliyense wosalandira Ufumu wa Mulungu ngati mwana wamngʼono sadzalowa nʼkomwe mu Ufumuwo.”+
3 Kenako anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, mukapanda kutembenuka*+ nʼkukhala ngati ana aangʼono, simudzalowa mu Ufumu wakumwamba.+
17 Ndithu ndikukuuzani, aliyense wosalandira Ufumu wa Mulungu ngati mwana wamngʼono sadzalowa nʼkomwe mu Ufumuwo.”+