Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 19:25, 26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ophunzirawo atamva zimenezi, anadabwa kwambiri ndipo anafunsa kuti: “Ndiye angapulumuke ndi ndani?”+ 26 Yesu anawayangʼanitsitsa nʼkuwauza kuti: “Kwa anthu zimenezi nʼzosatheka, koma zinthu zonse nʼzotheka kwa Mulungu.”+

  • Luka 18:26, 27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Amene anamva zimenezi anafunsa kuti: “Ndiye angapulumuke ndi ndani?”+ 27 Iye anawauza kuti: “Zinthu zosatheka kwa anthu nʼzotheka kwa Mulungu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena