Salimo 118:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala umene omanga nyumba anaukanaWakhala mwala wapakona* wofunika kwambiri.+ 23 Umenewu wachokera kwa Yehova,+Ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+
22 Mwala umene omanga nyumba anaukanaWakhala mwala wapakona* wofunika kwambiri.+ 23 Umenewu wachokera kwa Yehova,+Ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+