Mateyu 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo uthenga wabwino uwu wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni kwa anthu amitundu yonse,+ kenako mapeto adzafika. Aroma 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ndifunse kuti, Kodi kumva sanamve? Pajatu “mawu awo anamveka padziko lonse lapansi, ndipo uthenga wawo unamveka mpaka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.”+ Chivumbulutso 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinaona mngelo wina akuuluka chapafupi mumlengalenga. Iye anali ndi uthenga wabwino wosatha woti aulengeze kwa anthu amene akukhala padziko lapansi, kudziko lililonse, fuko lililonse, chilankhulo chilichonse ndi mtundu uliwonse.+
14 Ndipo uthenga wabwino uwu wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni kwa anthu amitundu yonse,+ kenako mapeto adzafika.
18 Koma ndifunse kuti, Kodi kumva sanamve? Pajatu “mawu awo anamveka padziko lonse lapansi, ndipo uthenga wawo unamveka mpaka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.”+
6 Ndinaona mngelo wina akuuluka chapafupi mumlengalenga. Iye anali ndi uthenga wabwino wosatha woti aulengeze kwa anthu amene akukhala padziko lapansi, kudziko lililonse, fuko lililonse, chilankhulo chilichonse ndi mtundu uliwonse.+