Mateyu 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zoonadi, Mwana wa munthu achoka, mogwirizana ndi zimene Malemba amanena za iye. Koma tsoka+ kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino kwa munthu ameneyu ngati akanapanda kubadwa.”+
24 Zoonadi, Mwana wa munthu achoka, mogwirizana ndi zimene Malemba amanena za iye. Koma tsoka+ kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino kwa munthu ameneyu ngati akanapanda kubadwa.”+