Luka 19:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo tsiku ndi tsiku iye anapitiriza kuphunzitsa mʼkachisimo. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu ankafunitsitsa kumupha.+ Yohane 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinkaphunzitsa mʼmasunagoge ndi mʼkachisi,+ kumene Ayuda onse ankasonkhana, ndipo sindinalankhule chilichonse kumbali.
47 Ndipo tsiku ndi tsiku iye anapitiriza kuphunzitsa mʼkachisimo. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu ankafunitsitsa kumupha.+
20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinkaphunzitsa mʼmasunagoge ndi mʼkachisi,+ kumene Ayuda onse ankasonkhana, ndipo sindinalankhule chilichonse kumbali.