59 Ndiyeno ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda ankafunafuna umboni wabodza kuti anamizire Yesu mlandu nʼcholinga choti amuphe.+ 60 Koma sanaupeze ngakhale kuti kunabwera mboni zambiri zabodza.+ Patapita nthawi, kunabwera mboni zina ziwiri