39 Chifukwa chimene chinachititsa kuti asakhulupirire nʼchimenenso Yesaya ananena kuti: 40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo, kuti asamaone ndi maso awowo, kuti mitima yawo isamvetse zinthu nʼkutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+