Mateyu 12:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Chifukwa aliyense amene amachita zimene Atate wanga wakumwamba amafuna, ameneyo ndi mchimwene wanga, mchemwali wanga ndi mayi anga.”+ Luka 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Poyankha Yesu anawauza kuti: “Mayi anga ndi azichimwene anga ndi awa amene amamvetsera mawu a Mulungu nʼkumawachita.”+ Yohane 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamachita zimene ndikukulamulani mukhala anzanga.+
50 Chifukwa aliyense amene amachita zimene Atate wanga wakumwamba amafuna, ameneyo ndi mchimwene wanga, mchemwali wanga ndi mayi anga.”+
21 Poyankha Yesu anawauza kuti: “Mayi anga ndi azichimwene anga ndi awa amene amamvetsera mawu a Mulungu nʼkumawachita.”+