Luka 1:57, 58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Tsopano nthawi yoti Elizabeti abereke inakwana ndipo anabereka mwana wamwamuna. 58 Anthu oyandikana naye komanso achibale ake anamva kuti Yehova* anamuchitira chifundo chachikulu ndipo anasangalala naye limodzi.+
57 Tsopano nthawi yoti Elizabeti abereke inakwana ndipo anabereka mwana wamwamuna. 58 Anthu oyandikana naye komanso achibale ake anamva kuti Yehova* anamuchitira chifundo chachikulu ndipo anasangalala naye limodzi.+