1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+ 1 Samueli 17:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, kodi bambo ako ndi ndani?” Davide anayankha kuti: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+ Mateyu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Jese anabereka Mfumu Davide.+ Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.
13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+
58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, kodi bambo ako ndi ndani?” Davide anayankha kuti: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+