Malaki 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzachititsa mitima ya abambo kubwerera kwa ana awo+ ndi mitima ya ana kubwerera kwa abambo awo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.”
6 Iye adzachititsa mitima ya abambo kubwerera kwa ana awo+ ndi mitima ya ana kubwerera kwa abambo awo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.”