Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 11:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chifukwa zonse zimene aneneri analemba komanso Chilamulo, zinalosera mpaka nthawi ya Yohane.+ 14 Kaya mukhulupirira kapena ayi, Yohane ndi ‘Eliya amene aneneri ananena kuti adzabwera.’+

  • Mateyu 17:10-12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma ophunzirawo anamufunsa kuti: “Nanga nʼchifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya ayenera kubwera choyamba?”+ 11 Iye anayankha kuti: “Inde, Eliya adzabweradi ndipo adzabwezeretsa zinthu zonse.+ 12 Komabe, ine ndikukuuzani kuti Eliya anabwera kale koma iwo sanamuzindikire ndipo anamuchitira zilizonse zimene iwo anafuna.+ Iwo adzazunzanso Mwana wa munthu mwa njira imeneyi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena