Mateyu 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atauza anthuwo kuti azipita, anakwera phiri yekhayekha kukapemphera.+ Iye anakhala kumeneko yekhayekha mpaka kunja kunada.
23 Atauza anthuwo kuti azipita, anakwera phiri yekhayekha kukapemphera.+ Iye anakhala kumeneko yekhayekha mpaka kunja kunada.