Yakobo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani inu anthu achuma. Lirani mofuula chifukwa cha masautso amene akubwera kwa inu.+