Mateyu 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni, inunso muwachitire zomwezo.+ Zimenezi ndi zomwe Chilamulo chimafuna komanso zimene aneneri analemba.+
12 Choncho zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni, inunso muwachitire zomwezo.+ Zimenezi ndi zomwe Chilamulo chimafuna komanso zimene aneneri analemba.+