Mateyu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamakhululukira anthu machimo awo, inunso Atate wanu wakumwamba adzakukhululukirani.+ Maliko 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo mukaimirira nʼkumapemphera, muzikhululuka chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireninso machimo anu.”+
25 Ndipo mukaimirira nʼkumapemphera, muzikhululuka chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireninso machimo anu.”+