Yakobo 1:23, 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa ngati munthu amangomva mawu koma osachita,+ amafanana ndi munthu amene akudziyangʼanira nkhope yake pagalasi. 24 Iye amadziyangʼana nʼkuchokapo ndipo nthawi yomweyo amaiwala kuti ndi munthu wotani.
23 Chifukwa ngati munthu amangomva mawu koma osachita,+ amafanana ndi munthu amene akudziyangʼanira nkhope yake pagalasi. 24 Iye amadziyangʼana nʼkuchokapo ndipo nthawi yomweyo amaiwala kuti ndi munthu wotani.