Mateyu 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno Yesu anayamba ulendo woyendera mizinda ndi midzi yonse. Iye ankaphunzitsa mʼmasunagoge awo komanso kulalikira uthenga wabwino wa Ufumu ndipo ankachiritsa matenda amtundu uliwonse amene anthu ankadwala.+ Luka 4:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Koma iye anawauza kuti: “Ndikuyenera kukalengezanso uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu kumizinda ina, chifukwa ndi zimene Mulungu anandituma kudzachita.”+
35 Ndiyeno Yesu anayamba ulendo woyendera mizinda ndi midzi yonse. Iye ankaphunzitsa mʼmasunagoge awo komanso kulalikira uthenga wabwino wa Ufumu ndipo ankachiritsa matenda amtundu uliwonse amene anthu ankadwala.+
43 Koma iye anawauza kuti: “Ndikuyenera kukalengezanso uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu kumizinda ina, chifukwa ndi zimene Mulungu anandituma kudzachita.”+