-
Chivumbulutso 20:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ nʼkumumanga kwa zaka 1,000. 3 Ndipo anamuponyera mʼphompho+ nʼkutseka pakhomo la phompholo kenako anaikapo chidindo kuti asasocheretsenso mitundu ya anthu mpaka zaka 1,000 zitatha. Pambuyo pake, adzamasulidwa kanthawi kochepa.+
-