Maliko 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atumwi anasonkhana kwa Yesu nʼkumuuza zonse zimene iwo anachita komanso kuphunzitsa.+