Mateyu 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Simoni Petulo anayankha kuti: “Ndinu Khristu,+ Mwana wa Mulungu wamoyo.”+ Maliko 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno anafunsa ophunzirawo kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Petulo anayankha kuti: “Ndinu Khristu.”+ Yohane 1:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choyamba iyeyu anakumana ndi mchimwene wake Simoni ndipo anamuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina limeneli akalimasulira limatanthauza, “Khristu”), Yohane 6:68, 69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Simoni Petulo anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu othandiza munthu kuti adzapeze moyo wosatha.+ 69 Ife takhulupirira ndipo tadziwa kuti inu ndinu Woyera amene Mulungu anamutumiza.”+
29 Ndiyeno anafunsa ophunzirawo kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Petulo anayankha kuti: “Ndinu Khristu.”+
41 Choyamba iyeyu anakumana ndi mchimwene wake Simoni ndipo anamuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina limeneli akalimasulira limatanthauza, “Khristu”),
68 Simoni Petulo anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu othandiza munthu kuti adzapeze moyo wosatha.+ 69 Ife takhulupirira ndipo tadziwa kuti inu ndinu Woyera amene Mulungu anamutumiza.”+