Mateyu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukalowa mumzinda kapena mʼmudzi uliwonse, muzifufuza yemwe ali woyenerera kumuuza uthenga wanu, ndipo muzikhala mʼnyumba yake mpaka nthawi yochoka.+ Luka 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukafika panyumba iliyonse, muzikhala mʼnyumbayo mpaka nthawi yochoka kumeneko itakwana.+
11 Mukalowa mumzinda kapena mʼmudzi uliwonse, muzifufuza yemwe ali woyenerera kumuuza uthenga wanu, ndipo muzikhala mʼnyumba yake mpaka nthawi yochoka.+