2 Samueli 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mumapulumutsa anthu odzichepetsa,+Koma mumanyansidwa ndi anthu odzikweza ndipo mumawatsitsa.+