Salimo 79:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tithandizeni inu Mulungu amene mumatipulumutsa,+Chifukwa cha dzina lanu laulemerero.Tipulumutseni komanso mutikhululukire* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+ Danieli 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Imvani, inu Yehova. Tikhululukireni,+ inu Yehova. Timvereni ndipo muchitepo kanthu, inu Yehova! Musazengereze inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu. Chifukwa mzinda wanu ndi anthu anu amadziwika ndi dzina lanu.”+
9 Tithandizeni inu Mulungu amene mumatipulumutsa,+Chifukwa cha dzina lanu laulemerero.Tipulumutseni komanso mutikhululukire* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+
19 Imvani, inu Yehova. Tikhululukireni,+ inu Yehova. Timvereni ndipo muchitepo kanthu, inu Yehova! Musazengereze inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu. Chifukwa mzinda wanu ndi anthu anu amadziwika ndi dzina lanu.”+