Mateyu 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno alembi ndi Afarisi ena anamupempha kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutionetse chizindikiro.”+ Maliko 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumeneku kunafika Afarisi ndipo anayamba kutsutsana naye. Ankafuna kuti iye awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba, pofuna kumuyesa.+
11 Kumeneku kunafika Afarisi ndipo anayamba kutsutsana naye. Ankafuna kuti iye awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba, pofuna kumuyesa.+