Genesis 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamʼpatse dzina lakuti Isaki.*+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, kuti likhale pangano losatha kwa mbadwa zake.+ Mika 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yakobo mudzamusonyeza kukhulupirika.Abulahamu mudzamusonyeza chikondi chokhulupirika,Ngati mmene munalumbirira kwa makolo athu kalekale.+ Agalatiya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano malonjezo anaperekedwa kwa Abulahamu ndi kwa mbadwa yake.*+ Malemba sanena kuti: “Kwa mbadwa zako,”* ngati kuti mbadwazo nʼzambiri. Koma akunena kuti, “kwa mbadwa yako,”* kutanthauza kuti ndi imodzi, amene ndi Khristu.+
19 Ndiyeno Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamʼpatse dzina lakuti Isaki.*+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, kuti likhale pangano losatha kwa mbadwa zake.+
20 Yakobo mudzamusonyeza kukhulupirika.Abulahamu mudzamusonyeza chikondi chokhulupirika,Ngati mmene munalumbirira kwa makolo athu kalekale.+
16 Tsopano malonjezo anaperekedwa kwa Abulahamu ndi kwa mbadwa yake.*+ Malemba sanena kuti: “Kwa mbadwa zako,”* ngati kuti mbadwazo nʼzambiri. Koma akunena kuti, “kwa mbadwa yako,”* kutanthauza kuti ndi imodzi, amene ndi Khristu.+