Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mfumukazi ya ku Sheba inamva za Solomo, zoti anatchuka chifukwa cha dzina la Yehova.+ Choncho inabwera kuti idzamuyese pomufunsa mafunso ovuta.+

  • 2 Mbiri 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mfumukazi ya ku Sheba+ inamva za Solomo. Choncho inabwera ku Yerusalemu kuti idzamuyese pomufunsa mafunso ovuta. Mfumukaziyo inapita ndi anthu ambiri oiperekeza. Inapita ndi ngamila zitanyamula mafuta a basamu, golide wambiri+ ndi miyala yamtengo wapatali. Inafika kwa Solomo nʼkuyamba kulankhula naye zonse zimene zinali mumtima mwake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena