Mateyu 23:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amakonda malo olemekezeka kwambiri pachakudya chamadzulo ndi mipando yakutsogolo* mʼmasunagoge.+ 7 Amakondanso kupatsidwa moni mʼmisika komanso kuti anthu aziwatchula kuti Rabi.*
6 Amakonda malo olemekezeka kwambiri pachakudya chamadzulo ndi mipando yakutsogolo* mʼmasunagoge.+ 7 Amakondanso kupatsidwa moni mʼmisika komanso kuti anthu aziwatchula kuti Rabi.*