Mateyu 10:26, 27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho musawaope, chifukwa palibe chobisika chimene sichidzaululika ndipo palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+ 27 Zimene ndimakuuzani mumdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunongʼonezana, muzilalikire muli padenga.+ Maliko 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa palibe chobisika chimene sichidzaululika ndipo palibe chimene chimasungidwa mwachinsinsi kwambiri chimene sichidzaululika.+ Luka 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa palibe chobisika chimene sichidzaululika. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika, sizidzabisika mpaka kalekale.+
26 Choncho musawaope, chifukwa palibe chobisika chimene sichidzaululika ndipo palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+ 27 Zimene ndimakuuzani mumdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunongʼonezana, muzilalikire muli padenga.+
22 Chifukwa palibe chobisika chimene sichidzaululika ndipo palibe chimene chimasungidwa mwachinsinsi kwambiri chimene sichidzaululika.+
17 Chifukwa palibe chobisika chimene sichidzaululika. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika, sizidzabisika mpaka kalekale.+