Mateyu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mpheta ziwiri amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu,* si choncho? Koma palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+
29 Mpheta ziwiri amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu,* si choncho? Koma palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+