Luka 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiye mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya chifukwa pemphero lako lopembedzera lamveka ndithu. Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamupatse dzina lakuti Yohane.+
13 Ndiye mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya chifukwa pemphero lako lopembedzera lamveka ndithu. Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamupatse dzina lakuti Yohane.+