-
Luka 1:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiye tamvera! Udzakhala chete osatha kulankhula, mpaka tsiku limene zinthu zimenezi zidzachitike chifukwa sunakhulupirire mawu anga amene adzakwaniritsidwe pa nthawi yake imene inaikidwiratu.”
-