Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 10:4-7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mfumukazi ya ku Sheba itaona nzeru zonse za Solomo,+ nyumba imene anamanga,+ 5 chakudya chapatebulo pake,+ operekera zakumwa, mmene atumiki ake ankakhalira pa nthawi ya chakudya, mmene operekera zakudya ankachitira komanso zovala zawo ndiponso nsembe zopsereza zimene ankapereka panyumba ya Yehova nthawi zonse, inasowa chonena. 6 Choncho inauza mfumuyo kuti: “Nkhani zimene ndinamva kudziko langa zokhudza zimene mwakwanitsa kuchita komanso nzeru zanu ndi zoona. 7 Koma sindinakhulupirire zimene ndinauzidwa mpaka pamene ndabwera nʼkuona ndi maso anga. Panopa ndaona kuti zimene ndinauzidwa zinali hafu chabe. Nzeru zanu ndi ulemerero wanu zaposa kwambiri zinthu zimene ndinamva.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena