Yohane 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndine mʼbusa wabwino. Nkhosa zanga ndimazidziwa ndipo nazonso zimandidziwa,+