Aefeso 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho khalani olimba, mutamanga kwambiri choonadi mʼchiuno mwanu ngati lamba,+ mutavala chodzitetezera pachifuwa chachilungamo,+ 1 Petulo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho konzekeretsani maganizo anu kuti mugwire ntchito mwamphamvu.+ Mukhalebe oganiza bwino+ ndipo muziyembekezera ndi mtima wonse kukoma mtima kwakukulu kumene adzakusonyezeni, Yesu Khristu akadzaonekera.*
14 Choncho khalani olimba, mutamanga kwambiri choonadi mʼchiuno mwanu ngati lamba,+ mutavala chodzitetezera pachifuwa chachilungamo,+
13 Choncho konzekeretsani maganizo anu kuti mugwire ntchito mwamphamvu.+ Mukhalebe oganiza bwino+ ndipo muziyembekezera ndi mtima wonse kukoma mtima kwakukulu kumene adzakusonyezeni, Yesu Khristu akadzaonekera.*