Mateyu 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ufumu wakumwamba tingauyerekezere ndi anamwali 10 amene anatenga nyale zawo+ nʼkupita kukachingamira mkwati.+ Afilipi 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezerani komanso osalakwa. Mukhale ana a Mulungu+ opanda chilema pakati pa mʼbadwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota.+ Pakati pa mʼbadwo umenewu inu mukuwala ngati zounikira mʼdzikoli.+
25 “Ufumu wakumwamba tingauyerekezere ndi anamwali 10 amene anatenga nyale zawo+ nʼkupita kukachingamira mkwati.+
15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezerani komanso osalakwa. Mukhale ana a Mulungu+ opanda chilema pakati pa mʼbadwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota.+ Pakati pa mʼbadwo umenewu inu mukuwala ngati zounikira mʼdzikoli.+