Mateyu 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa aliyense amene ali nazo, adzapatsidwa zinanso zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka. Koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+ Yohane 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amadula nthambi iliyonse mwa ine imene sikubereka zipatso ndipo iliyonse imene ikubereka zipatso amaiyeretsa poitengulira kuti ibereke zipatso zambiri.+
29 Chifukwa aliyense amene ali nazo, adzapatsidwa zinanso zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka. Koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
2 Iwo amadula nthambi iliyonse mwa ine imene sikubereka zipatso ndipo iliyonse imene ikubereka zipatso amaiyeretsa poitengulira kuti ibereke zipatso zambiri.+