Yohane 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Moyo wanga ukuvutika tsopano,+ kodi ndinene chiyani? Atate ndipulumutseni ku nthawi yovutayi.+ Komabe nthawi imeneyi ikuyenera kundifikira pakuti nʼchifukwa chake ndinabwera.
27 Moyo wanga ukuvutika tsopano,+ kodi ndinene chiyani? Atate ndipulumutseni ku nthawi yovutayi.+ Komabe nthawi imeneyi ikuyenera kundifikira pakuti nʼchifukwa chake ndinabwera.