Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndidzasunga pangano limene ine ndachita ndi iwe+ komanso ndi mbadwa zako* mʼmibadwo yawo yonse. Lidzakhala pangano losatha kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbadwa zako.

  • Levitiko 26:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Choncho ndidzakumbukira pangano limene ndinachita ndi Yakobo,+ Isaki+ komanso Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo.

  • Salimo 106:45, 46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Pofuna kuwathandiza iye ankakumbukira pangano lake,

      Ndipo ankawamvera chisoni* chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika chomwe ndi chachikulu.*+

      46 Iye ankachititsa kuti anthu onse amene anawagwira ukapolo+

      Awamvere chisoni.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena