Mateyu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya mzimu wa Mulungu, ndiye kuti Ufumu wa Mulungu wakufikirani modzidzimutsa.+ Mateyu 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Uzani mwana wamkazi wa Ziyoni* kuti: ‘Taona! Mfumu yako ikubwera kwa iwe.+ Ndi yofatsa+ ndipo yakwera bulu, yakwera mwana wamphongo wa bulu, mwana wa nyama yonyamula katundu.’”+
28 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya mzimu wa Mulungu, ndiye kuti Ufumu wa Mulungu wakufikirani modzidzimutsa.+
5 “Uzani mwana wamkazi wa Ziyoni* kuti: ‘Taona! Mfumu yako ikubwera kwa iwe.+ Ndi yofatsa+ ndipo yakwera bulu, yakwera mwana wamphongo wa bulu, mwana wa nyama yonyamula katundu.’”+