Genesis 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kutatsala pangʼono kucha, angelowo anayamba kumuuza Loti kuti afulumire. Iwo anamuuza kuti: “Fulumira! Tenga mkazi wako ndi ana ako aakazi awiriwa, kuti musawonongedwe limodzi ndi mzindawu chifukwa cha kulakwa kwake.”+
15 Kutatsala pangʼono kucha, angelowo anayamba kumuuza Loti kuti afulumire. Iwo anamuuza kuti: “Fulumira! Tenga mkazi wako ndi ana ako aakazi awiriwa, kuti musawonongedwe limodzi ndi mzindawu chifukwa cha kulakwa kwake.”+