Mateyu 24:40, 41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pa nthawiyo, amuna awiri adzakhala ali mʼmunda. Mmodzi adzatengedwa ndipo winayo adzasiyidwa. 41 Akazi awiri adzakhala akupera pamphero. Mmodzi adzatengedwa ndipo winayo adzasiyidwa.+
40 Pa nthawiyo, amuna awiri adzakhala ali mʼmunda. Mmodzi adzatengedwa ndipo winayo adzasiyidwa. 41 Akazi awiri adzakhala akupera pamphero. Mmodzi adzatengedwa ndipo winayo adzasiyidwa.+