Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 118:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova.+

      Tikupempha kuti Yehova akudalitseni mʼnyumba yake.

  • Mateyu 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Komanso gulu la anthu limene linali patsogolo pake ndi mʼmbuyo mwake linkafuula kuti: “Mʼpulumutseni Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova!*+ Mʼpulumutseni kumwambamwambako!”+

  • Maliko 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno amene anali patsogolo komanso amene ankabwera mʼmbuyo ankafuula kuti: “Mʼpulumutseni!+ Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova!*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena